Matthew 4:15 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Iwe dziko la Zebuloni ndi iwe dziko la Nafutali, ku njira yakunyanja, patsidya pa Yordani, iwe Galileya, dziko la anthu akunja!
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Dziko la Zebuloni ndi dziko la Nafutali, njira ya kunyanja, kutsidya lija la Yordani, Galileya la anthu akunja,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Dziko la Zebuloni ndi dziko la Nafutali, njira ya ku nyanja, kutsidya lija la Yorodani, Galileya wa anthu a mitundu ina,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
It Dziko la Zebuloni ndi dziko la N afitali, Njira ya kunyanja, kutsidya lija la Yordano, Galileya la anthu akunja,