Matthew 4:2 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pa masiku makumi anai Yesu adasala zakudya usana ndi usiku, ndipo pambuyo pake adamva njala.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo pamene Iye analibe kudya masiku makumi anai usana ndi usiku, pambuyo pake anamva njala.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo atasala kudya masiku makumi anayi usana ndi usiku, anamva njala.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo pamene Iye analibe kudya masiku makumi anai usana ndi usiku, pambuyo pace anamva njala.