Matthew 5:31 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Anthu akale aja adaaŵalamulanso kuti, ‘Ngati munthu asudzula mkazi wake, ampatse mkaziyo kalata yachisudzulo.’
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Kunanenedwanso, Yense wakuchotsa mkazi wake ampatse iye chilekaniro:
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Ananena kuti, ‘Aliyense wosudzula mkazi wake ayenera amupatse kalata ya chisudzulo.’
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kunanenedwanso, Yense wakucotsa mkazi wace 3 ampatse iye cilekaniro: