Matthew 5:33 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Mudamvanso kuti anthu akale aja adaaŵalamula kuti, ‘Usalumbire monama, koma uchitedi zimene udaŵalonjeza Ambuye molumbira.’
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndiponso, munamva kuti kunanenedwa kwa iwo akale, Usalumbire konama, koma udzapereka kwa Ambuye zolumbira zako:
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Munamvanso kuti kunanenedwa kwa anthu akale kuti, ‘Musaphwanye lonjezo; koma sungani malonjezo anu amene mwachita kwa Yehova.’
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndiponso, munamva kuti kunanenedwa kwa iwo akale, 5 Usalumbire konama, koma udzapereka kwa Ambuye zolumbira zako: