Matthew 5:38 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Mudamva kuti anthu akale aja adaaŵalamula kuti, ‘Diso kulipa diso, dzino kulipa dzino.’
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Munamva kuti kunanenedwa, Diso kulipa diso, ndi dzino kulipa dzino:
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Munamva kuti, ‘Diso kulipira diso ndi dzino kulipira dzino.’
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Munamva kuti kunanenedwa, 10 Diso kulipa diso, ndi dzino kulipa dzino: