Matthew 5:43 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Mudamva kuti anthu akale aja adaaŵalamula kuti, ‘Ukonde mnzako, ndi kudana ndi mdani wako.’
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Munamva kuti kunanenedwa, Uzikondana ndi mnansi wako, ndi kumuda mdani wako:
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Munamva kuti, ‘Konda mnansi wako ndi kudana ndi mdani wako.’
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Munamva kuti kunanenedwa, 14 Uzikondana ndi mnansi wako, ndi kumuda mdani wako: