Matthew 5:48 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Nchifukwa chake monga Atate anu akumwamba ali abwino kotheratu, inunso mukhale abwino kotheratu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chifukwa chake inu mukhale angwiro, monga Atate wanu wa Kumwamba ali wangwiro.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Nʼchifukwa chake, inu khalani angwiro monga Atate anu akumwamba ali wangwiro.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Cifukwa cace inu 18 mukhale angwiro, monga Atate wanu wa Kumwamba ali wangwiro.