Matthew 5:6 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ngodala anthu amene akumva njala ndi ludzu lofuna chilungamo, pakuti Mulungu adzakwaniritsa zofuna zao.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Odala ali akumva njala ndi ludzu la chilungamo; chifukwa adzakhuta.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Odala ndi amene akumva njala ndi ludzu la chilungamo, chifukwa adzakhutitsidwa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Odala ali akumva njala ndi ludzu la cilungamo; cifukwa adzakhuta.