Matthew 5:7 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ngodala anthu ochitira anzao chifundo, pakuti iwonso Mulungu adzaŵachitira chifundo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Odala ali akuchitira chifundo; chifukwa adzalandira chifundo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Odala ndi amene ali ndi chifundo, chifukwa adzawachitira chifundo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Odala ali akucitira cifundo; cifukwa adzalandira cifundo.