Matthew 6:27 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndani mwa inu ndi maganizo ankhaŵa angathe kuwonjezera ngakhale tsiku limodzi pa moyo wake?
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo ndani wa inu ndi kudera nkhawa angathe kuonjezera pa msinkhu wake mkono umodzi?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kodi ndani wa inu podandaula angathe kuwonjeza ora limodzi pa moyo wake?
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo ndani wa inu ndi kudera nkhawa angathe kuonjezera pa msinkhu wace mkono umodzi?