Matthew 8:17 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adachita zimenezi kuti zipherezere zimene mneneri Yesaya adaanena zakuti, “Iye adatenga zofooka zathu, adasenza nthenda zathu.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
kotero kuti chikwaniridwe chonenedwa ndi Yesaya mneneri, kuti, Iye yekha anatenga zofooka zathu, nanyamula nthenda zathu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Uku kunali kukwaniritsa zimene ananena mneneri Yesaya kuti, “Iye anatenga zofowoka zathu, nanyamula nthenda zathu.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
kotero kuti cikwaniridwe conenedwa ndi Yesaya mneneri, kuti, Iye yekha anatenga zofoka zathu, Nanyamula nthenda zathu.