Matthew 8:6 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adampempha kuti, “Ambuye, wantchito wanga ali gone kunyumbaku. Sakutha kuyenda, ndipo akumva kupweteka kwambiri.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
nati, Ambuye, mnyamata wanga ali gone m'nyumba wodwala manjenje, wozunzidwa koopsa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
nati, “Ambuye, wantchito wanga ali chigonere ku nyumba, sakuthanso kuyenda, akumva kuwawa kwambiri.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
nati, Ambuye, mnyamata wanga ali gone m'nyumba wodwala manjenje, wozunzidwa koopsa,