Matthew 9:21 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mumtima mwake ankaganiza kuti, “Ndikangokhudza ngakhale chovala chake chokhacho, ndichira.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
pakuti analikunena mwa iye yekha, Ngati ndingakhudze chofunda chake chokha ndidzachira.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iyeyo anati mwa iye yekha, “Nditangokhudza kasonga ka mkanjo wake, ine ndidzachiritsidwa.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
pakuti analikunena mwa iye yekha, Ngati ndingakhudze copfunda cace cokha ndidzacira.