Matthew 9:37 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono adauza ophunzira ake kuti, “Dzinthu ndzochulukadi, achepa ndi antchito.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pomwepo ananena kwa ophunzira ake, Zotuta zichulukadi koma antchito ali owerengeka.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pamenepo anati kwa ophunzira ake, “Zokolola ndi zambiri koma antchito ndi ochepa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pomwepo ananena kwa ophunzira ace, Zotuta zicurukadi koma anchito ali owerengeka.