Matthew 9:7 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Munthu uja adadzukadi namapita kwao.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo ananyamuka, napita kunyumba kwake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo munthuyo anayimirira napita kwawo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo ananyamuka, napita ku nyumba kwace.