Micah 1:14 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono a ku Moreseti-Gati mutsazikane nawo. Anthu a ku Akizibu adzanamiza mafumu a ku Israele.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chifukwa chake pereka mphatso zolawirana kwa Moreseti-Gati; nyumba za Akizibu zidzakhala chinthu chabodza kwa mafumu a Israele.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Chifukwa chake perekani mphatso zolawirana ndi a ku Moreseti Gati. Mzinda wa Akizibu udzaonetsa kunama kwa mafumu a Israeli.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Cifukwa cace pereka mphatso zolawirana kwa Moreseti Gati; nyumba za Akizibi zidzakhala cinthu cabodza kwa mafumu a Israyeli.