Micah 1:15 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Inunso anthu a ku Maresa, ndidzakutumirani adani kuti akugonjetseni. Akuluakulu a ku Israele adzabisala m'thanthwe la Adulamu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndidzakutengeranso wokhala m'Maresa iwe, iye amene adzakulandira ukhale cholowa chake; ulemerero wa Israele udzafikira ku Adulamu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndidzabweretsa mgonjetsi kudzalimbana ndi inu okhala mu Maresa. Ulemerero wa Israeli udzafika ku Adulamu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndidzakutengeranso wokhala m'Maresa iwe, iye amene adzakulandira ukhale colowa cace; ulemerero wa Israyeli udzafikira ku Adulamu.