Micah 1:2 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Imvani nonsenu anthu a mitundu yonse. Tchera khutu iwe dziko lapansi ndi zonse zokhala m'menemo. Ambuye Chauta akuimbani mlandu, akulankhulira ku Nyumba yao yoyera.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Imvani, mitundu ya anthu, inu nonse; tamvera, dziko lapansi, ndi zonse zili m'mwemo; ndipo Ambuye Yehova akhale mboni yakutsutsa inu, Ambuye m'Kachisi wake wopatulika.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Tamverani, inu anthu a mitundu yonse, mvetsera iwe dziko lapansi ndi okhala mʼmenemo, pakuti Ambuye Yehova achitira umboni wokutsutsani, Ambuye akuyankhula ali mʼnyumba yake yopatulika.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Imvani, mitundu ya anthu, inu nonse; tamvera, dziko lapansi, ndi zonse ziri m'mwemo; ndipo Ambuye Yehova akhale mboni yakutsutsa inu, Ambuye m'Kacisi wace wopatulika.