Micah 1:9 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Samariya, zilonda za uchimo wake sizingathe kupola, zafika mpaka ku Yuda. Chiwonongeko chili pafupi ndi mzinda wa anthu anga, chafika mpaka ku Yerusalemu kwenikweni.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti mabala ake ndi osapola; pakuti afikira ku Yuda; afikira ku chipata cha anthu anga, ku Yerusalemu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pakuti chilonda cha Samariya nʼchosachizika; chafika ku Yuda. Chafika pa chipata chenicheni cha anthu anga, mpaka mu Yerusalemu mwenimwenimo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti mabala ace ndi osapola; pakuti afikira ku Yuda; afikira ku cipata ca anthu anga, ku Yerusalemu.