Micah 3:7 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Alauli adzaŵanyazitsa, oombeza maula adzaŵachititsa manyazi. Onse adzangoti pakamwa gwirire, chifukwa Mulungu sakuŵayankha.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo alauli adzachita manyazi, ndi olosa adzathedwa nzeru; ndipo onsewo adzasunama; pakuti kuyankha kwa Mulungu kulibe.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Alosi adzachita manyazi ndipo owombeza mawula adzanyazitsidwa. Onse adzaphimba nkhope zawo chifukwa Mulungu sakuwayankha.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo alauli adzacita manyazi, ndi olosa adzathedwa nzeru; ndipo onsewo adzasunama; pakuti kuyankha kwa Mulungu kulibe.