Micah 4:5 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mitundu yonse ya anthu imayenda, uliwonse m'njira ya mulungu wake; koma ife tidzayenda m'njira ya Chauta, Mulungu wathu, mpaka muyaya.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti mitundu yonse ya anthu idzayenda, wonse m'dzina la mulungu wake, ndipo ife tidzayenda m'dzina la Yehova Mulungu wathu kunthawi yonka muyaya.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mitundu yonse ya anthu itha kutsatira milungu yawo; ife tidzayenda mʼnjira za Yehova Mulungu wathu mpaka muyaya.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti mitundu yonse ya anthu idzayenda, wonse m'dzina la mlungu wace, ndipo ife tidzayenda m'dzina la Yehova Mulungu wathu ku nthawi yomka muyaya.