Micah 6:12 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Anthu olemera amachita zankhondo. Anthu onse ndi abodza, amangokhalira kunama.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti anthu ake olemera adzala ndi chiwawa, ndi okhalamo amanena bodza, ndi lilime lao limachita monyenga m'kamwa mwao.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Anthu ake olemera amachita zachiwawa; anthu ake ndi abodza ndipo pakamwa pawo pamayankhula zachinyengo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti anthu ace olemera adzala ndi ciwawa, ndi okhalamo amanena bodza, ndi lilime lao limacita monyenga m'kamwa mwao.