Micah 6:13 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Nchifukwa chake ndayambapo kukukanthani, kukuwonongani chifukwa cha machimo anu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chifukwa chake Inenso ndakukantha ndi kukupweteketsa; ndakupulula chifukwa cha zochimwa zako.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Choncho, ndayamba kukuwonongani, kukusakazani chifukwa cha machimo anu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Cifukwa cace Inenso ndakukantha ndi kukupweteketsa; ndakupulula cifukwa ca zocimwa zako.