Micah 6:3 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chauta akuti, “Inu anthu anga, kodi ndakuchitani chiyani? Kodi ndakutopetsani nchiyani? Tandiyankhani!
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Anthu anga inu, ndakuchitirani chiyani? Ndakulemetsani ndi chiyani? Chitani umboni wonditsutsa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Anthu anga, kodi ndakuchitirani chiyani? Kodi ndakutopetsani bwanji? Ndiyankheni.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Anthu anga inu, ndakucitirani ciani? ndakulemetsani ndi ciani? citani umboni wonditsutsa.