Micah 6:9 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndi nzeru kuwopa dzina la Chauta. Akuuza mzinda wa Yerusalemu kuti, “Imvani, inu anthu onse okhala mumzinda muno.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mau a Yehova aitana mudzi, ndi wanzeru aopa dzina lanu; tamverani ndodo, ndi Iye amene anaiika.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Tamverani! Yehova akuyitana anthu okhala mu mzinda ndi nzeru kuopa dzina lanu. “Mverani mfumu ndi Iye amene anayikhazikitsa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mau a Yehova aitana mudzi, ndi wanzeru aopa dzina lanu; tamverani ndodo, ndi Iye amene anaiika.