Micah 7:11 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Inu anthu a ku Yerusalemu, idzafikatu nthaŵi yomanganso malinga anu. Nthaŵi imeneyo malire anu adzafutuzidwa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Tsiku lakumanga malinga ako, tsiku lomwelo lembalo lidzachotsedwa kunka kutali.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Idzafika nthawi yomanganso makoma anu, nthawi yokulitsanso malire anu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Tsiku lakumanga malinga ako, tsiku lomwelo lembalo lidzacotsedwa kunka kutali.