Micah 7:13 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma dziko lapansi lidzasanduka chipululu chifukwa cha zoipa za anthu ake. Amenewo ndiwo malipiro a ntchito zao.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma dziko lidzakhala labwinja chifukwa cha iwo okhalamo, mwa zipatso za machitidwe ao.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Dziko lapansi lidzasanduka chipululu chifukwa cha anthu okhala mʼdzikomo, potsatira zochita za anthuwo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma dziko lidzakhala labwinja cifukwa ca iwo okhalamo, mwa zipatso za macitidwe ao.