Micah 7:15 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chauta akuti, “Ndidzaŵaonetsa zodabwitsa, monga masiku amene ankatuluka ku Ejipito.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Monga masiku a kutuluka kwako m'dziko la Ejipito ndidzamuonetsa zodabwitsa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Ndidzawaonetsa zodabwitsa zanga, ngati masiku amene ndinawatulutsa mʼdziko la Igupto.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Monga masiku a kuturuka kwako m'dziko la Aigupto ndidzamuonetsa zodabwitsa.