Micah 7:20 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mudzaonetsa kukhulupirika kwanu kwa Yakobe, ndi chikondi chanu chosasinthika kwa Abrahamu, monga mudalonjezera molumbira kwa makolo athu kuyambira pa masiku amakedzana.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mudzapatsa kwa Yakobo choonadi, ndi kwa Abrahamu chifundo chimene munalumbirira makolo athu kuyambira masiku a kale lomwe.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mudzakhala wokhulupirika kwa Yakobo, ndi kuonetsa chifundo chanu kwa Abrahamu, monga munalonjeza molumbira kwa makolo athu masiku amakedzana.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mudzapatsa kwa Yakobo coonadi, ndi kwa Abrahamu cifundo cimene munalumbirira makolo athu kuyambira masiku a kale lomwe.