Nahum 1:10 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adzaŵatentha kotheratu ngati ziyangoyango za minga ndiponso ngati ziputu zouma.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti chinkana akunga minga yoyangayanga, naledzera nacho choledzeretsa chao, adzathedwa konse ngati chiputu chouma.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iwo adzakodwa mu ziyangoyango za minga ndipo adzaledzera ndi vinyo wawo; adzatenthedwa ngati ziputu zowuma.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti cinkana akunga minga yoyangayanga, naledzera naco coledzeretsa cao, adzathedwa konse ngati ciputu couma.