Nahum 1:11 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ku Ninive kudachokera munthu wa cholinga choipa, wofuna kuchita Chauta chiwembu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mwa iwe watuluka wina wolingalira choipa chotsutsana ndi Yehova, ndiye phungu wopanda pake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kwa iwe, Ninive, kunachokera munthu wa cholinga choyipa, wofuna kuchitira Yehova chiwembu, amene amapereka uphungu woyipa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mwa iwe waturuka wina wolingalira coipa cotsutsana ndi Yehova, ndiye phungu wopanda pace.