Nahum 1:4 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Akangoilamula nyanja, imauma, amaumitsanso mitsinje yonse. Zomera za ku Basani ndi za ku Karimele zimauma, maluŵa a ku Lebanoni amafota.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Adzudzula nyanja, naiphwetsa, naumitsa mitsinje yonse; Basani ndi Karimele afota, ndi duwa la ku Lebanoni linyala.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Amalamulira nyanja ndipo imawuma; amawumitsa mitsinje yonse. Zomera za ku Basani ndi Karimeli zimawuma ndipo maluwa a ku Lebanoni amafota.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Adzudzula nyanja, naiphwetsa, naumitsa mitsinje yonse; Basana ndi Karimeli afota, ndi duwa la ku Lebano linyala.