Nahum 1:8 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma ndi madzi achigumula adzaononga adani ake, ndipo adzaŵapirikitsira ku malo amdima.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma ndi chigumula chosefukira adzatha konse malo ake, nadzapirikitsira adani ake kumdima.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
koma ndi madzi achigumula choopsa Iye adzawononga adani ake (Ninive); adzapirikitsira adani ake ku malo a mdima.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma ndi cigumula cosefukira adzatha konse malo ace, nadzapitikitsira adani ace kumdima.