Nahum 2:1 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Inu a ku Ninive, othira nkhondo akubwera kudzakuwonongani. Ikani ankhondo pa malinga! Muziyang'ana ku mseu! Konzekerani nkhondo! Valani dzilimbe!
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Wophwanyayo wakwera pamaso pako; sunga linga, yang'anira panjira, limbitsa m'chuuno mwako, limbikitsatu mphamvu yako.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Wodzathira nkhondo akubwera kudzalimbana nawe, Ninive. Tetezani malinga anu, dziyangʼanani ku msewu, konzekerani nkhondo, valani dzilimbe.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Wophwanyayo wakwera pamaso pako; sunga linga, yang'anira panjira, limbitsa m'cuuno mwako, limbikitsatu mphamvu yako.