Nahum 2:5 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Atsogoleri a ankhondo akuitanidwa, akubwera naphunthwa. Akuthamangira ku linga la mzinda, akuimika chipupa chodzitetezera.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Akumbukira omveka ake; akhumudwa m'kupita kwao, afulumira kulinga lake, ndi chotchinjiriza chakonzeka.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iye akuyitanitsa asilikali ake wolemekezeka, koma iwo akubwera napunthwa. Akuthamangira ku linga la mzinda; akuyimika chodzitchinjirizira pamalo pake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Akumbukila omveka ace; akhumudwa m'kupita kwao, afulumira ku linga lace, ndi cocinjiriza cakonzeka.