Nahum 2:7 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mfumukazi yake yatengedwa ukapolo. Adzakazi ake akulira ngati nkhunda, ndipo akudzigunda pa chifuwa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chatsimikizika, avulidwa, atengedwa, adzakazi ake alira ngati mau a nkhunda, nadziguguda pachifuwa pao.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Zatsimikizika kuti mzinda utengedwa ndi kupita ku ukapolo. Akapolo aakazi akulira ngati nkhunda ndipo akudziguguda pachifuwa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Catsimikizika, abvulidwa, atengedwa, adzakazi ace alira ngati mau a nkhunda, nadziguguda pacifuwa pao.