Nahum 2:8 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ninive wasanduka ngati chidziŵe, chimene madzi ake ali faa kutuluka. Ena akufuula kuti, “Imani! Imani!” Koma palibe amene akubwerera.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma Ninive wakhala chiyambire chake ngati thamanda lamadzi; koma athawa. Imani, Imani! Ati, koma palibe wocheuka.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ninive ali ngati dziwe, ndipo madzi ake akutayika. Iwo akufuwula kuti, “Imani! Imani!” Koma palibe amene akubwerera.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma Nineve wakhala ciyambire cace ngati thamanda lamadzi; koma athawa. Imani, Imani! ati, koma palibe woceuka.