Nahum 3:1 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsoka kwa mzinda wokhetsa magazi a anthu ambiri, mzinda wodzaza ndi mabodza ndi zakuba, wokonda kufunkha mosalekeza.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Tsoka mudzi wa mwazi! Udzala nao mabodza ndi zachifwamba; zachifwamba sizidukiza.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Tsoka kwa mzinda wopha anthu, mzinda wodzaza ndi mabodza, mzinda wodzaza ndi anthu olanda zinthu anzawo, mu mzinda mʼmene simusowa anthu osautsidwa nthawi zonse!
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Tsoka mudzi wa mwazi! udzala nao mabodza ndi zacifwamba; zacifwamba sizidukiza.