Nahum 3:13 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ankhondo ako ali ngati akazi. Zipata za dziko lako zaŵatsekukira adani ako, ndipo moto wapsereza mipiringidzo yake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Taona, anthu ako m'kati mwako akunga akazi, zipata za dziko lako zatsegulidwira adani ako papakulu; moto watha mipingiridzo yako.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Tayangʼana ankhondo ako, onse ali ngati akazi! Zipata za dziko lako zatsekukira adani ako; moto wapsereza mipiringidzo yake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Taona, anthuako m'kati mwako akunga akazi; zipata za dziko lako zatsegulidwira adani ako papakuru; moto watha mipingiridzo yako.