Nahum 3:16 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mudachulukitsa anthu anu amalonda kupambana nyenyezi zamumlengalenga. Koma onsewo adamwazikana ngati dzombe.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Wachulukitsa amalonda ako koposa nyenyezi za kuthambo; chirimamine anyambita, nauluka, nathawa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mwachulukitsa chiwerengero cha anthu a malonda anu mpaka kupambana nyenyezi za mlengalenga, koma iwo ngati dzombe akuwononga dziko ndipo kenaka akuwuluka nʼkuchoka.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Wacurukitsa amalonda ako koposa nyenyezi za kuthambo; cirimamine anyambita, nauluka, nathawa.