Nahum 3:7 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndipo onse okuwona adzakuthaŵa, adzati, ‘Ninive wasanduka bwinja, adzamlira ndani?’ Ndidzamtenga kuti woti akusangalatse?” Akuterotu Chauta.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo kudzali kuti onse akupenyerera iwe adzakuthawa, nadzati, Ninive wapasuka, adzamlira maliro ndani? Ndidzakufunira kuti akukutonthoza?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Onse amene adzakuona adzakuthawa ndipo adzati, ‘Ninive wasanduka bwinja, adzamulira ndani?’ Kodi ndingamupeze kuti munthu woti nʼkukutonthoza?”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo kudzali kuti onse akupenyerera iwe adzakuthawa, nadzati, Nineve wapasuka, adzamlira maliro ndani? ndidzakufunira kuti akukutonthoza?