Nahum 3:8 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kodi iwe Ninive ndiwe wopambana Thebesi? Suja mzinda umenewu unali m'mbali mwa mtsinje wa Nailo utazingidwa ndi madzi. Madziwo anali ngati khoma lake ndi linga lake?
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Kodi uli wabwino woposa No-Amoni, wokhala pakati pa mitsinje wozingidwa ndi madzi; amene tchemba lake ndilo nyanja, ndi linga lake ndilo nyanja?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kodi ndiwe wopambana Tebesi, mzinda wokhala mʼmbali mwa Nailo, wozunguliridwa ndi madzi? Mtsinjewo unali chitetezo chake, madziwo anali linga lake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kodi uli wabwino woposa No-Amoni, wokhala pakati pa mitsinje wozingidwa ndi madzi; amene chemba lace ndilo nyanja, ndi linga lace ndilo nyanja?