Nehemiah 1:10 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Iwoŵa ndiwo atumiki anu ndi anthu anu amene mudaŵapulumutsa ndi mphamvu yanu yaikulu ndi dzanja lanu lolimba.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo awa ndi akapolo anu ndi anthu anu, amene munawaombola ndi mphamvu yanu yaikulu, ndi dzanja lanu lolimba.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Iwo ndi atumiki anu ndi anthu anu, amene munawawombola ndi mphamvu yanu yayikulu ndi dzanja lanu lamphamvu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo awa ndi akapolo anu ndi anthu anu, amene munawaombola ndi mphamvu yanu yaikuru, ndi dzanja lanu lolimba.