Nehemiah 1:8 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kumbukirani mau amene mudauza Mose mtumiki wanu akuti, ‘Ngati mukhala osakhulupirika, ndidzakumwazani pakati pa anthu a mitundu ina.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mukumbukire mau mudalamulira mtumiki wanu Mose, ndi kuti, Mukalakwa, ndidzakubalalitsani mwa mitundu ya anthu;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Kumbukirani mawu amene munawuza mtumiki wanu Mose akuti, ‘Ngati mukhala osakhulupirika, ndidzakubalalitsani pakati pa mitundu ina.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mukumbukile mau mudalamulira mtumiki wanu Mose, ndi kuti, Mukalakwa, ndidzakubalalitsani mwa mitundu ya anthu;