Nehemiah 10:1 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Anthu amene adasindikiza chidindo chao movomereza chipanganocho ndi aŵa: Nehemiya, bwanamkubwa uja, mwana wa Hakaliya, Zedekiya,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Okomera chizindikiro tsono ndiwo Nehemiya, Tirisata mwana wa Hakaliya, ndi Zedekiya,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Amene anasindikiza chidindo anali awa: Nehemiya, bwanamkubwa uja, mwana wa Hakaliya. Zedekiya,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Okomera cizindikilo tsono ndiwo Nehemiya, Tirisata mwana wa Hakaliya, ndi Zedekiya,