Nehemiah 10:35 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tikulonjezanso kuti tidzabwera ndi zipatso zoyamba kucha za kuminda kwathu, ndi zipatso zoyamba kucha za mtengo uliwonse wazipatso, chaka ndi chaka, kuti tizipereke ku Nyumba ya Chauta.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndi kubwera nazo zipatso zoyamba za nthaka, ndi zoyamba za zipatso zonse za mtengo uliwonse chaka ndi chaka, ku nyumba ya Yehova;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Tilonjezanso kuti tidzabwera ndi zipatso zoyamba kucha za mʼminda yathu ndi zipatso zoyamba kucha za mtengo uliwonse wa zipatso chaka ndi chaka kuti tidzapereke ku Nyumba ya Mulungu wathu.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndi kubwera nazo zipatso zoyamba za nthaka, ndi zoyamba za zipatso zonse za mtengo uli wonse caka ndi caka, ku nyumba ya Yehova;