Nehemiah 10:9 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Alevi anali aŵa: Yesuwa mwana wa Azaniya, Binuyi, wa fuko la Henadadi, Kadimiyele,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndi Alevi ndiwo Yesuwa mwana wa Azaniya, Binuyi wa ana a Henadadi, Kadimiyele;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Alevi anali awa: Yesuwa mwana wa Azaniya, Binuyi wa fuko la Henadadi, Kadimieli,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndi Alevi ndiwo Yesuwa mwana wa Azaniya, Binui wa ana a Henadadi, Kadiniyeli;