Nehemiah 11:24 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono Petahiya, mwana wa Mesezabele, mmodzi mwa adzukulu a Sera wa m'fuko la Yuda, ankaimirira Aisraele ku bwalo la mfumu ya ku Persiya.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndi Petahiya mwana wa Mesezabele, wa ana a Zera, mwana wa Yuda, anatumikira mfumu pa milandu yonse ya anthuwo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Petahiya mwana wa Mesezabeli, mmodzi mwa zidzukulu za Zera mwana wa Yuda ndiye ankayimirira Aisraeli pa bwalo la mfumu ya Perisiya.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndi Petatiya mwana wa Mesezabele, wa ana a Zera, mwana wa Yuda, anatumikira mfumu pa mirandu yonse ya anthuwo.