Nehemiah 11:25 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Anthu ena a fuko la Yuda ankakhala ku Kiriyati-Ariba ndi midzi yake, ku Diboni ndi midzi yake, ku Yekabizeele ndi midzi yake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndi ana ena a Yuda anakhala m'midzi ya kuminda yao, m'Kiriyati-Ariba ndi milaga yake, ndi m'Diboni ndi milaga yake, ndi m'Yekabizeele ndi midzi yake,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Anthu ena a fuko la Yuda ankakhala ku Kiriyati-Ariba ndi midzi yake, ku Diboni ndi midzi yake, ku Yekabizeeli ndi midzi yake,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndi ana ena a Yuda anakhala m'midzi ya ku minda yao, m'Kiriyati Ariba ndi miraga yace, ndi m'Diboni ndi miraga yace, ndi m'Yekabizeeli ndi midzi yace,