Nehemiah 11:28 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ena ankakhala ku Zikilagi, ku Mekona ndi midzi yake,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndi m'Zikilagi, ndi m'Mekona ndi milaga yake,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ku Zikilagi, Mekona ndi midzi yawo,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndi m'Zikilaga, ndi m'Mekona ndi miraga yace,